Genesis 4:5 BL92

5 koma sanayang'anira Kaini ndi nsembe yace. Kaini ndipo anakwiya kwambiri, niigwa nkhope yace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 4

Onani Genesis 4:5 nkhani