5 Ndipo anagona nalotanso kaciwiri: ndipo taonani, ngala zisanu ndi ziwiri za tirigu zinamera pa mbuwa imodzi, zonenepa ndi zabwino.
Werengani mutu wathunthu Genesis 41
Onani Genesis 41:5 nkhani