Genesis 42:16 BL92

16 Tumizani mmodzi wa inu akatenge, adze naye mphwanu: ndipo inu mudzamangidwa kuti mau anu ayesedwe, ngati zoona ziri mwa inu: penatu, pali moyo wa Farao, muli ozonda ndithu.

Werengani mutu wathunthu Genesis 42

Onani Genesis 42:16 nkhani