Genesis 42:33 BL92

33 Ndipo munthuyo mwini dziko anati kwa ife, Momwemu ndidzadziwa kuti muli anthu oona; siyani mmodzi wa abale anu pamodzi ndi ine, tengani tirigu wa njala ya kwanu, mukani;

Werengani mutu wathunthu Genesis 42

Onani Genesis 42:33 nkhani