Genesis 44:15 BL92

15 Ndipo losefe anati kwa iwo, Ici nciani nwacicita? Kodi simudziwa kuti nunthu ngati ine ndingathe kuzindidra ndithu?

Werengani mutu wathunthu Genesis 44

Onani Genesis 44:15 nkhani