Genesis 44:18 BL92

18 Ndipo Yuda anayandikira kwa iye nati, Mfumu, kapolo wanu aneneretu m'makutu a mbuyanga, mtima wanu usapse pokwiya ndi kapolo wanu; cifukwa muli ngati Farao.

Werengani mutu wathunthu Genesis 44

Onani Genesis 44:18 nkhani