Genesis 45:10 BL92

10 Ndipo mudzakhala m'dziko la Goseni, mudzakhala pafupi ndi ine, inu ndi ana anu, ndi ana a ana anu, ndi nkhosa zanu, ndi zoweta zanu, ndi zonse muli nazo;

Werengani mutu wathunthu Genesis 45

Onani Genesis 45:10 nkhani