24 Ndipo anamukitsa abale ace, ndipo anacoka; ndipo anati kwa iwo, Musakangane panjira.
Werengani mutu wathunthu Genesis 45
Onani Genesis 45:24 nkhani