Genesis 45:4 BL92

4 Ndipo Yosefe anati kwa abale ace, Muyandikiretu kwa ine; nayandikira. Ndipo iye anati, Ine ndine Yosefe mbale wanu, ine ndemwe munandigulitsa ndilowe m'Aigupto.

Werengani mutu wathunthu Genesis 45

Onani Genesis 45:4 nkhani