1 Ndipo Israyeli anamuka ulendo wace ndi zonse anali nazo, nafika ku Beereseba, napereka nsembe kwa Mulungu wa Isake atate wace.
Werengani mutu wathunthu Genesis 46
Onani Genesis 46:1 nkhani