Genesis 46:12 BL92

12 Ndi ana amuna a Yuda: Eri, ndi Onani, ndi Sela, ndi Perezi, ndi Zera; koma Eri ndi Onani anafa m'dziko la Kanani. Ndi ana amuna a Perezi ndiwo Hezroni ndi Hamuli.

Werengani mutu wathunthu Genesis 46

Onani Genesis 46:12 nkhani