18 Amenewa ndi ana a Zilipa, amene Labani anampatsa Leya mwana wace wamkazi, amenewo anambalira Yakobo, anthu khumi ndi asanu ndi mmodzi.
Werengani mutu wathunthu Genesis 46
Onani Genesis 46:18 nkhani