25 Amenewa ndi ana a Biliha, amene Labani anampatsa Rakele mwana wace wamkazi, amenewo anambalira Yakobo; anthu onse ndiwo asanu ndi awiri.
Werengani mutu wathunthu Genesis 46
Onani Genesis 46:25 nkhani