Genesis 47:15 BL92

15 Ndipo zitatha ndalama zonse m'dziko la Aigupto ndi m'dziko la Kanani, Aaigupto onse anadza kwa Yosefe, nati, Mutipatse ife cakudya; tiferenji pamaso panu? zatsirizika ndalama.

Werengani mutu wathunthu Genesis 47

Onani Genesis 47:15 nkhani