Genesis 48:15 BL92

15 Ndipo anadalitsa Yosefe, nati, Mulungu, pamaso pace anayenda makolo anga Abrahamu ndi Isake, Mulungu amene anandidyetsa ine nthawi zonse za moyo wanga kufikira lero,

Werengani mutu wathunthu Genesis 48

Onani Genesis 48:15 nkhani