10 Ndodo yacifumu siidzacoka mwa Yuda,Kapena wolamulira pakati pa mapazi ace,Kufikira atadza Silo;Ndipo anthu adzamvera iye.
Werengani mutu wathunthu Genesis 49
Onani Genesis 49:10 nkhani