33 Pamene Yakobo anatha kulangiza ana ace amuna, anafunya mapazi ace pakama, natsirizika, nasonkhanizidwa kwa anthu a mtundu wace.
Werengani mutu wathunthu Genesis 49
Onani Genesis 49:33 nkhani