21 Ndipo tsopano musaope; Ine ndidzacereza inu, ndi ana anu ang'ono. Ndipo anawatonthoza iwo mitima yao, nanena nao mokoma mtima.
Werengani mutu wathunthu Genesis 50
Onani Genesis 50:21 nkhani