26 Ndipo anafa Yosefe, anali wa zaka zana limodzi ndi khumi; ndipo anakonza thupi lace ndi mankhwala osungira, ndipo ariamuika iye m'bokosi m'Aigupto.
Werengani mutu wathunthu Genesis 50
Onani Genesis 50:26 nkhani