Genesis 7:19 BL92

19 Ndipo madzi anapambana ndithu pa dziko lapansi; anamizidwa mapiri atari onse amene anali pansi pa thambo lonse.

Werengani mutu wathunthu Genesis 7

Onani Genesis 7:19 nkhani