Genesis 7:2 BL92

2 Nyama zonse zodyedwa udzitengereko wekha zisanu ndi ziwiri, zisanu ndi ziwiri, yamphongo ndi yaikazi yace; ndi nyama zosadyedwa ziwiri ziwiri yamphongo ndi yaikazi yace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 7

Onani Genesis 7:2 nkhani