Genesis 9:10 BL92

10 ndi zamoyo zonse ziti pamodzi ndi inu, zouluka, ng'ombe, ndi zinyama zonse za dziko lapansi, pamodzi ndi inu; zonse zoturuka m'cingalawa, zinyama zonse za dziko lapansi,

Werengani mutu wathunthu Genesis 9

Onani Genesis 9:10 nkhani