Ezekieli 10:7 BL92

7 Pamenepo kerubi wina anatambasula dzanja lace pakati pa akerubi ku moto uli pakati pa akerubi, naparako, nauika m'manja mwa iye wobvala bafuta, ndiye naulandita, naturuka.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 10

Onani Ezekieli 10:7 nkhani