24 Ndipo mzimu unandikweza, nufika nane m'masomphenya mwa mzimu wa Mulungu ku dziko la Akasidi, kwa andendewo. M'mwemo masomphenya ndidawaona anandicokera, nakwera.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 11
Onani Ezekieli 11:24 nkhani