Ezekieli 11:5 BL92

5 Pamenepo mzimu wa Yehova unandigwera, ndipo ananti kwa ine, Nena, Atero Yehova, Mwatero nyumba ya Israyeli, pakuti ndidziwa zimene zimalowa m'mtima mwanu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 11

Onani Ezekieli 11:5 nkhani