9 Ndipo ndidzakuturutsani m'kati mwace, ndi kukuperekani m'manja a alendo, ndi kucita maweruzo pakati panu.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 11
Onani Ezekieli 11:9 nkhani