Ezekieli 12:10 BL92

10 Unene nao, Atero Ambuye Yehova, Katundu uyu anena za kalonga wa m'Yerusalemu, ndi nyumba yonse ya Israyeli yokhala pakati pao.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 12

Onani Ezekieli 12:10 nkhani