Ezekieli 12:12 BL92

12 Kalongayo ali pakati pao adzasenza paphewa pace mumdima, nadzaturuka; adzaboola palinga, nadzaturutsapo; adzaphimba nkhope yace kuti asapenye dziko ndi maso ace.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 12

Onani Ezekieli 12:12 nkhani