Ezekieli 12:16 BL92

16 Koma ndidzawasiya owerengeka apulumuke lupanga, ndi njala, ndi mliri, kuti afotokoze zonyansa zao kwa amitundu kumene afikako; ndipo adzadziwa kuti Ine ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 12

Onani Ezekieli 12:16 nkhani