Ezekieli 12:25 BL92

25 Pakuti Ine ndine Yehova, ndidzanena, ndi mau ndidzanenawo adzacitika, osazengerezekanso; pakuti m'masiku anu, nyumba yopanduka inu, ndidzanena mau ndi kuwacita, ati Yehova Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 12

Onani Ezekieli 12:25 nkhani