Ezekieli 13:11 BL92

11 uziti nao olimata ndi dothi losapondeka, kuti lidzagwa, lidzabvumbidwa ndi mvula yaikuru; ndi inu, matalala akuru, mudzagwa; ndi mkuntho udzalithithimula.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 13

Onani Ezekieli 13:11 nkhani