Ezekieli 13:13 BL92

13 Cifukwa cace atero Ambuye Yehova, Ndidzalithithimula ndi mkuntho m'ukali wanga; ndipo lidzabvumbidwa ndi mvula yaikuru mu mkwiyo wanga, ndi matalala akuru adzalitha m'ukali wanga.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 13

Onani Ezekieli 13:13 nkhani