Ezekieli 13:22 BL92

22 Popeza mwamvetsa cisoni ndi mabodza mtima wa wolungama, amene sindinamvetsa cisoni Ine, ndi kumlimbitsa manja woipa, kuti asabwerere kuleka njira yace yoipa, ndi kusungidwa wamoyo;

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 13

Onani Ezekieli 13:22 nkhani