Ezekieli 14:16 BL92

16 cinkana anthu omwewo atatu akadakhala m'mwemo, Pali Ine, ati Ambuye Yehova, sakadapulumutsa ana amuna kapena akazi; iwo akadapulumuka okha; koma dziko likadakhala lacipululu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 14

Onani Ezekieli 14:16 nkhani