Ezekieli 14:20 BL92

20 cinkana Nowa, Danieli, ndi Yobu, akadakhala m'mwemo, Pali Ine, ati Ambuye Yehova, sakadapulumutsa ana amuna kapena akazi; akadapulumutsa moyo wao wokha ndi cilungamo cao.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 14

Onani Ezekieli 14:20 nkhani