6 Cifukwa cace uziti kwa nyumba ya Israyeli, Atero Ambuye Yehova, Bwerani, lekani mafano anu, tembenuzani nkhope zanu kuzisiya zonyansa zanu zonse.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 14
Onani Ezekieli 14:6 nkhani