Ezekieli 14:9 BL92

9 Ndipo akaceteka mneneriyo, nakanena mau, Ine Yehova ndamceta mneneri uja; ndipo ndidzamtambasulira dzanja langa, ndi kumuononga pakati pa anthu anga Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 14

Onani Ezekieli 14:9 nkhani