22 Ndipo pa zonyansa zako zonse ndi zigololo zako sunakumbukila masiku a ubwana wako, mujaunakhala wamarisece ndi wausiwa, wobvimvinizika m'mwazi wako.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 16
Onani Ezekieli 16:22 nkhani