Ezekieli 16:25 BL92

25 Unamanga ciunda cako pa mphambano ziri zonse, ndipo unanyansitsa kukongola kwako, ndi kutukula mapazi ako kwa yense wopitako, ndi kucurukitsa cigololo cako.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 16

Onani Ezekieli 16:25 nkhani