Ezekieli 16:3 BL92

3 Atero Ambuye Yehova kwa Yerusalemu, Ciyambi cako ndi kubadwa kwako ndiko ku dziko la Akanani; atate wako anali M-amori, ndi mai wako Mhiti.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 16

Onani Ezekieli 16:3 nkhani