33 Anthu amaninkha akazi onse acigololo mphatso, koma iwe umaninkha mabwenzi ako onse mphatso zako ndi kuwalipira, kuti akudzere kucokera ku mbali zonse, kuti acite nawe cigololo.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 16
Onani Ezekieli 16:33 nkhani