Ezekieli 16:5 BL92

5 Panalibe diso linakucitira cifundo, kukucitira cimodzi conse ca izi, kucitira iwe nsoni; koma unatayidwa kuyere; pakuti ananyansidwa nao moyo wako tsiku la kubadwa kwake,

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 16

Onani Ezekieli 16:5 nkhani