Ezekieli 17:15 BL92

15 Koma anapandukira ndi kutuma mithenga yace ku Aigupto, kuti ampatse akavalo ndi anthu ambiri. Adzapindula kodi? adzapulumuka wakucita izi? atyole pangano ndi kupulumuka kodi?

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 17

Onani Ezekieli 17:15 nkhani