Ezekieli 18:19 BL92

19 Koma inu mukuti, Alekeranji mwana kusenza mphulupulu za atate wace? Mwanayo akacita ciweruzo ndi cilungamo, nakasunga malemba anga onse, ndi kuwacita, adzakhala ndi moyo ndithu.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 18

Onani Ezekieli 18:19 nkhani