21 Koma woipayo akabwerera kusiya macimo ace onse adawacita nakasunga malemba anga onse, ndi kucita ciweruzo ndi cilungamo, adzakhala ndi moyo ndithu, sadzafa.
Werengani mutu wathunthu Ezekieli 18
Onani Ezekieli 18:21 nkhani