Ezekieli 18:23 BL92

23 Ngati ndikondwera nayo imfa ya woipa? ati Ambuye Yehova, si ndiko kuti abwerere kuleka njira yace, ndi kukhala ndi moyo?

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 18

Onani Ezekieli 18:23 nkhani