Ezekieli 18:29 BL92

29 Koma nyumba ya Israyeli imanena, Njira ya Ambuye njosayenera, Inu, nyumba ya Israyeli, kodi njira zanga nzosayenera? njira zanu si ndizo zosayenera?

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 18

Onani Ezekieli 18:29 nkhani