Ezekieli 18:31 BL92

31 Tayani, ndi kudzicotsera zolakwa zanu zonse zimene munalakwa nazo, ndi kudzifunira mtima watsopano, ndi mzimu watsopano; pakuti mudzaferanji inu, nyumba ya Israyeli?

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 18

Onani Ezekieli 18:31 nkhani