Ezekieli 19:12 BL92

12 Koma unazulidwa mwaukali, unaponyedwa pansi ndi mphepo ya kum'mawa, inaumitsa zipatso zace, ndodo zace zolimba zinatyoka ndi kuuma, moto unazitha.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 19

Onani Ezekieli 19:12 nkhani