Ezekieli 19:5 BL92

5 Pakuona tsono waukaziwo, kuti unalindirira, ndi kuti ciyembekezo cace cidatha, unatenga wina wa ana ace, numsandutsa msona.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 19

Onani Ezekieli 19:5 nkhani